Thupi la Malemu Khansala Rams Kajosolo wa Ntiya Ward mu Mzinda wa Zomba yemwe adali wachipani cha UTM layikidwa mmanda lero kumudzi kwao ku Mdeka kwa T/A Chigalu Boma la Blantyre. Poyankhula pamwambo woyika m’manda thupili, wofalitsa nkhani kuchipani cha UTM a Felix Njawala adati mtsogoleri wachipachi Saulosi Chilima yemwenso ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko […]
The post Thupi la Khansala Kajosolo wa ku Zomba layikidwa m’manda appeared first on Malawi24.