…wati sanayitanidwe ndi Mulungu kuzafusira akazi …wapemphelera mbiyang’ambe kuti zisiye kumwa mowa …wapempha akufuna kwabwino kuti amusamutse m’nyumba yake ya K6000 akalowe ya K30,000 “Onetsa lavu mami”: mneneri wamakono ano yemwe wazula mitima ya anthu ochuluka, Habakkuk, wati akulandira mayeselo ofusilidwa ndi atsikana ndipo wati ndichifukwa chake anachitchaja chiphadzuwa china K10,000 kuti chisiye kuwavutitsa. Mneneri […]
The post Atsikana akumandifusira kwambiri, ndinatchaja ndalama kuti asapitilize – mneneri Habakkuk appeared first on Malawi24.