Kwavuta ku Mwanza: anthu akugonana kwambiri, sakudziteteza

Pamene boma komaso mabungwe osiyanasiyana akulimbikitsa kuti anthu azigwiritsa ntchito njira zozitetezera pogonana, zadziwika kuti m’boma la Mwanza sizili choncho, chiwerengero cha odwala matenda opatsirana poganana chakwera kwambiri. Izi ndimalingana ndi a Samuel Simbi amene ndi m’modzi mwa madotolo akuluakulu pa chipatala cha Mwanza omwe amayankhula ndi imodzi mwa nyumba zofalitsira mawu m’dziko muno. A […]

The post Kwavuta ku Mwanza: anthu akugonana kwambiri, sakudziteteza appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください