Tabitha Chawinga yemwe ndi katswiri posewera mpira wa miyendo wati iye adzayamba kuganiza zokwatiwa akadzafika zaka makumi atatu (30). Chawinga yemweso ndi mtsogoleri wa osewera mpira wa miyendo ya atsikana ya dziko lino ya Scorchers, amayankhula izi pomwe amacheza ndi wailesi ya Malawi Broadcasting Corporation (MBC). Osewerayu yemwe posachedwepa wakhala mtsikana oyamba mu Africa kumwetsa […]
The post Sindikukwatiwa pano – Tabitha Chawinga appeared first on Malawi24.