Ndege ya ufiti yagwa m’boma la Balaka

Khwimbi la anthu m’dera la Mangerengere Mfumu yaikulu Kapalamula m’boma la Balaka lachiwiri m’mawa lidakhamukira pa nyumba ina pomwe pagwa chinthu china chodabwitsa m’maonekedwe ndipo akukhulupilira kuti chinthucho ndi ndege ya ufiti. Chinthu chodabwitsacho chomwe ndi lichero lomwe muli mikanda, mafupa a nyama komanso nyama yowoneka kuti yongodzongedwa kumene akuti chapezedwa panja pa chipata cha […]

The post Ndege ya ufiti yagwa m’boma la Balaka appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください