Kuli kanthu konthala nchala pa zisankho za mu 2025; nduna ya za maboma ang’ono a Richard Chimwendo Banda akuti timu yowina sumayichotsa mgalaundi ndipo anenetsa kuti sakuona chipani chomwe chingamugwedeze Lazarus Chakwera. Izi zalankhulidwa lamulungu pa 18 June, 2023 pomwe akuluakulu angapo a chipani cha Malawi Congress (MCP) anachititsa msonkhano wa ndale pa sukulu ya […]
The post Chakwera wabwera kudzakhala, palibe angamuchotse – Chimwendo Banda appeared first on Malawi24.