Ndilibe ulamuliro onse wa boma – Chakwera

Mtsogoleri wa dziko la Malawi a Lazarus Chakwera wati anthu ena akufuna kuti iye akhale ndi mphavu zonse pa ntchito za m’boma zomwe wati ndikusemphana ndi malamulo. A Chakwera anena izi Lolemba pa 12 June, 2023 pomwe amatsekulira msonkhano wa masiku awiri wokhudza kulekanitsidwa kwa mphamvu za ulamuliro womwe ukuchitikira ku Bingu International Convention Centre […]

The post Ndilibe ulamuliro onse wa boma – Chakwera appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください