Zikukhala ngati oyimba m’dziko muno apeza golide ku America pomwe naye Patience Namadingo watengeka mtima ndi ulendo wa Lulu, ndipo naye wati akupita kukaimba ku South Bend, ku ‘mang’ina’ kuja. Posachedwapa, oyimba angapo kuphatikizapo Lawrence ‘Lulu’ Khwisa, Limbani ‘Tay Grin’ Kalirani ndi ena, anapita m’dziko la mkaka ndi uchili komwe onsewa anaimba malo angapo. Kupita […]
The post Namadingo wa ku South Bend, ku mang’ina appeared first on Malawi24.