Bwanamkubwa wa boma la Balaka, Darwin Mngoli, wati anthu ogwira ntchito mu nthambi zosiyanasiyana za boma mu khonsolo ya Balaka alandira malipiro awo a mwezi wa May pakutha pa tsiku la lero, lolemba pa 5 June 2023. A Mngoli anena izi pakutha pa mkumano omwe adali nawo ndi nthumwi zoyimira ogwira ntchito za boma pa […]
The post Ogwira ntchito za Boma ku Balaka alonjezedwa kulandira malipiro awo lero appeared first on Malawi24.