Yemwe anayamba maimbidwe ngati oyimba nyimbo zauzimu Patience Namadingo, watekesa pa masamba anchezo kaamba ka kanema yemwe akumuonetsa akubisa botolo la mowa. Kanema ina yomwe anthu akugawana pa masamba anchezo ikumuonetsa Namadingo ataima ndi mzake Cassim Ibrahim yemwe wayimba naye nyimbo ya ‘Sadziwa’ yomweso ambiri akuikonda. Mukanemayi yomwe yajambulidwa awiriwa ataima pachinthu china chomwe chimazungulira, […]
The post Tchimo kuzuza: Namadingo abisa botolo la mowa appeared first on Malawi24.