Ogwira ntchito mu nthambi zosiyanasiyana za boma ku khonsolo ya Balaka mam’mawa uno akhamukira ku ofesi za Khonsolo ya bomali ati kamba ka kusakondwa ndi kuchedwa kwa malipiro a mwezi wa May. Ogwira ntchitowa ati akufunanso mayankho kuchokera kwa akuluakulu a khonsoloyi pa chomwe chimachititsa kuti nthawi zonse azichedwa kulandira malipiro awo a pamwezi. M’modzi […]
The post Ogwira ntchito ku khonsolo ya Balaka akwiya ndi kuchedwa kwa malipiro appeared first on Malawi24.