Pamene vuto lakuvuta kwa madzi lafika tsiku lachisanu mu mzinda wa Zomba, mabwalo amilandu ayamba ayimitsa ntchito zawo tsopano. Malawi24 itakayendera Bwalo la Chief Resident Magistrate komanso Bwalo lalikulu la Zomba High Court tidapeza ntchito zoweruza milandu zitayimitsidwa. Izi zapangitsa kuti anthu omwe adatsekeredwa poganidziridwa kuti apalamula milandu yawupandu ndipo akuyembekezera kuti akawonekere kubwalo lamilandu […]
The post Mabwalo amilandu ayimitsa ntchito zawo ku Zomba chifukwa cha vuto la madzi appeared first on Malawi24.