Vera Kadwale wa zaka 10 yemwe amachokera m’mudzi wa Ngomano, Mfumu yaikulu Chimatiro M’boma la Balaka ndipo salankhula komanso kuyenda akufunika thandizo la njinga yoyendera anthu a ulumali. Vera akukanika akusangalala ndi maufulu osiyanasiyana omwe ana anzake amakhala nawo monga ufulu wa maphunziro ndi kusewera kamba kosowa njinga yoyendera anthu a ulumali. Vera, yemwe ali ndi […]
The post Vera wa zaka 10 ku Balaka akufunika thandizo la njinga yoyendera anthu a ulumali appeared first on Malawi24.