Apolisi awaphunzitsa momwe angachepetsere nkhanza zokhudza kugonana

Wachiwiri kwa mkulu woona chitetedzo cha m’madera akumidzi kunthambi ya a Police m’dziko muno Senior Supritendent Albert Nyongani wapempha a Police kuti adziyendera kawirikawiri malo (misasa) omwe anthu okhudzidwa ndi ngozi zokugwa mwadzidzidzi amakhala pofuna kuthana ndi nkhanza zokhudza kugonana komanso nkhanza zina zomwe anthuwa amakumana nazo. Supritendent Nyongani amayankhula izi ku Police ya Machinga […]

The post Apolisi awaphunzitsa momwe angachepetsere nkhanza zokhudza kugonana appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください