Nyabingi Sambo: Peter wayamba za chamba cha lege

M’khalakale pamaimbidwe Peter Sambo wati chamba cha lege chomwe wayamba kuyimba pano, chimuthandiza kuti afikile anthu ochuluka ndi uthenga wabwino kuposa momwe amayimba nyimbo zauzimu. Nkhaniyi ikutsatira kubwera poyera kwa oyimbayu ndikulengeza kuti kuyambira tsopano sadziyimba nyimbo zauzimu zokhazokha pomwe wakhazikitsa chamba chake chatsopano chomwe akuchitchula kuti ‘Afro-reggae’. Sambo wati ngakhale kuti kuyambira pano sakhazikika […]

The post Nyabingi Sambo: Peter wayamba za chamba cha lege appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください