Gulu la Dzuka Malawi likufuna Atupele akhalenso mtsogoleri wa UDF

Pomwe pangotsala chaka chimodzi kuti Chipani cha United Democratic Front (UDF) chichititse msonkhano wake waukulu osankha komiti yatsopano yoyendetsa chipanichi, gulu lina lomwe likudzitchula kuti Dzuka Malawi labwera poyera kufuna kuti Atupele Muluzi akhale mtsogoleri wachipanichi. Poyankhula pa msonkhano wa atolankhani ku Gymkhana Club mu mzinda wa Zomba, Msungichuma wamkulu wagulu la Dzuka Malawi Isaac […]

The post Gulu la Dzuka Malawi likufuna Atupele akhalenso mtsogoleri wa UDF appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください