Pomwe akuluakulu a kampani ya Ichocho Power Security (IPS) anali kuwunguzawunguza kuti nsuzi uzipezeka bwanji ngati kampaniyi ingalandidwe chiphaso, boma labweza ganizo lake pa nkhaniyi. Nkhaniyi inayamba sabata imodzi yapitayo pomwe mkulu wa IPS a Yassin ‘Ichocho’ Suwedi anazijambura ndikutulutsa kanema momwe anauza a Jai Banda kuti agwira ndikusunga mokaka miza mwana wawo Tonderai. Suwedi […]
The post Pita koma usakachimweso; boma lakhululukira Ichocho appeared first on Malawi24.