Oyimba wa mdziko la DRC Awilo Longomba washosha mavu nkhomola kaamba kodya ndalama ya oyimba wa ku Malawi Lawi. Awilo ankati abwera kudzaimba koma sanabwere ndipo pano sakuyankha foni. Kuyambira chaka chatha, oyimba Francis Chris Phiri yemwe amadziwika kwambiri kuti Lawi, wakhala akukozekera phwando la maimbidwe lomwe likuyenera kuchitika lero ku Bingu International Conference Center […]
The post Awilo watokosola aMalawi podya ndalama ya Lawi appeared first on Malawi24.