…150 miliyoni ya anthu inasokonekera…musamvere zachambazo – akutero Kachamba Ngwira Inu amene mumaziona mutatsegula kampani zanu za sopo, kaya kupanga shuga, enanu ma juwisi ndi zimzake, iwalani zimenezo. Mkulu analonjeza zokhutitsa a Malawi ndi luso la mu mafakitale, a Kondwani Kachamba Ngwira, awatengera ku bwalo. Ati adyera anthu ochuluka amene ankakhulupilira malonjezo awo aja. Malinga […]
The post Wadzetsa chisoni Kondwani: amusumira Kachamba Ngwira appeared first on Malawi24.