Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wakhululukira Mussa John yemwe chaka chatha analamulidwa kukakhala ku ndende kwa zaka zitatu atapezeka olakwa pa mlandu opezeka ndi chamba. Nduna ya za mdziko a Zikhale Ng’oma atsimikiza kuti John ndi m’modzi wa akaidi 200 omwe akhululukidwa potengera nyengo ino yokumbukira kufa ndi kuuka kwa Ambuye Yesu. John anapezeka […]
The post Chakwera wakhululukira Mussa John appeared first on Malawi24.