…Wadzudzula mchitidwe ozithandiza wekha Kudya beti ndi kosangalatsa inde. Kwa ena kupambana mayeso kumene kutha kukhala chinthu cha mtengo wa pamwamba. Koma zonsezi sizingafike pa kugonana. Kugonana ndicho chinthu chokongola kwambiri pa dziko pano, watero mtsogoleri wa mpingo wa katolika pa dziko lonse, Papa. Malinga ndi pologalamu ya padera imene ikupezeka pa Disney +, mtsogoleri […]
The post Muli uthenga mu kugonana. Ndi chinthu chokongola kwambiri – watero Papa appeared first on Malawi24.