…boma likupanga malamulo atsopano okhaulitsa ma dalaiva a chakumwa Phungu wa dera la pakati mu boma la Mwanza a Nicolas Dausi anachemetsa ku nyumba ya malamulo pamene anadzudzula nduna ya boma kuti imanyogodola anthu omwa mowa kuwatchula kuti ndi zidakwa. A Dausi anati iwo monga mkulu wa chakumwa, mawu awa sanawakhalire bwino. Mdando wa a […]
The post Osatitchula zidakwa, mowa timamwela kusangalala basi – watero mbiyang’ambe Dausi appeared first on Malawi24.