Kapinga wa bwana asamanyentchere: boma laika K1.1 biliyoni yosamalilira maluwa ku nyumba yachifumu

Pamene boma la Malawi limati lilibe ndalama zothandizira aMalawi mazana mazana omwe akhudzidwa ndi ngozi ya madzi osefukira, boma lomwelo laika ndalama yokwana K1.1 biliyoni kuti igwiritsidwe ntchito posamalira maluwa ndi kapinga ku nyumba yachifumu. Izi zili mu ndondomeko ya za chuma ya chaka chino mpaka chaka chamawa yomwe boma la Malawi lati ligwiritsa ntchito […]

The post Kapinga wa bwana asamanyentchere: boma laika K1.1 biliyoni yosamalilira maluwa ku nyumba yachifumu appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください