Senior Chief Malemia yathokoza chifukwa chowakwezera mafumu malipiro

Senior Chief Malemia ya boma la Zomba yathokoza boma chifukwa chokwezera mafumu malipiro ndipo ati izi zipangitsa kuti mafumu azilimbikira ntchito. Senior Chief Malemia yawuza Malawi24 kuti mafumu andodo a Boma la Zomba akondwera kwambiri chifukwa poyamba amalandira swahala wochepa kwambiri. Iwo ati mafumu amagwira ntchito yotamandika kwambiri m’madera momwe amakhala choncho kukwezeredwa swahala kupangitsa […]

The post Senior Chief Malemia yathokoza chifukwa chowakwezera mafumu malipiro appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください