Bodza lonamiza dziko kumati mafuta atsika mtengo mu December lija ati amapitilira nalo. Ati amanamizanso amayi osiyanasiyana amene tikunena pano ndi oyembekezera. Anawaimikawo ati ndi a nduna ofatsa aja a Sosten Gwengwe. Munthu wina wamayi wavula gule pagulu atabwera pa tsamba la mchezo la Facebook kufotokoza kuti iye wakhala akuzemberana ndi nduna ya za chuma […]
The post Atangwa kuvundukula ma siketi uku mmalo mokonza chuma: mzimayi wayalutsa Gwengwe appeared first on Malawi24.