Mbiyang’ambe zogwa nawo zili ku CCAP

Ngakhale mpingo wa CCAP umaletsa kumwa mowa, kafukufuku wasonyeza kuti akhilisitu ampingo wa CCAP mumzinda wa Lilongwe ndi omwe amamwa mowa kwambiri ngati kulibe mawa. Kafukufuku wasonyeza kuti zidakwa zochuluka mumzinda wa Lilongwe ndi akhilisitu amene amapemphera mpingo wa Church of Central African Presbyterian (CCAP) pomwe mipesa ili pa nambala ya chisanu (5). Izi ndi […]

The post Mbiyang’ambe zogwa nawo zili ku CCAP appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください