Anthu ena omwe akhudzidwa ndi namondwe wa Freddy ndipo akukhala mmalo oyembekezera, awuza anthu akufuna kwabwino omwe akumakawazonda kuti asamawapititsire tchipisi ndi chiboda cha nkhuku, koma bolako nsima. Izi ndi malingana ndi kanema amene anthu akugawana m’masamba a nchezo amene akuwonetsa mzibambo mmodzi okhudzidwa ndi namondwe wa Freddy akuuza mtolankhani wina kuti iwo sakufuna tchipisi […]
The post Tikufuna nsima osati tchipisi, adandaula anthu kumisasa appeared first on Malawi24.