Asilikali awiri apamadzi sakupezeka ku Mulanje

Asilikali awiri omwe amafuna kupulumutsa anthu ena omwe akhudzidwa ndi madzi osefukira m’boma la Mulanje, sakupezeka. Malingana ndi nduna ya za ma boma a Richard Chimwendo Banda omwe ali pa Mkando m’boma la Mulanje, asilikali atatu a pamadzi ananyamuka pa bwato ndicholinga chofuna kukapulumutsa anthu ena omwe anali pamwamba pa malo othilira mafuta agalimoto. Malipoti […]

The post Asilikali awiri apamadzi sakupezeka ku Mulanje appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください