A Malawi kuchulukana ngati mchenga: ana 1,628 abadwa tsiku la khisimisi lokha

Pokwanilitsa mau omwe amapezeka m’buku lopatulika pa Genesesi 1 ndime ya 28, lomwe limati; ‘Mulungu ndipo anadalitsa iwo, ndipo adati kwa iwo, Mubalane, mucuruke, mudzaze dziko lapansi,’ zadziwika kuti ana okwana 1,628 ndi omwe abadwa mdziko muno tsiku la khisimisi lokha. Izi ndi malingana ndichikalata chomwe unduna wa zaumoyo watulutsa sabata ino chomwe chasonyeza kuti […]

The post A Malawi kuchulukana ngati mchenga: ana 1,628 abadwa tsiku la khisimisi lokha appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください