Pamene anthu ena pa dziko lonse lapansi akhala akutsutsana kwa nthawi yaitali ngati palidi njoka za zikazi kapena za zimuna komaso ngati za zikazizo zilidi ndi maliseche oyipangitsa kuti izimva kukoma zikamagonana, akatswiri a sayasi ku Australia apeza kuti njoka za zikazi zilinso ndi mikongo ngati anthu ndi nyama zina. Akatswiri a sayasiwa omwe ndiochokera […]
The post Njoka yayikazi ili ndi maliseche achizimai – atero akatswiri appeared first on Malawi24.