Khirisimisi isakuloweni mnthumba – atero Papa

Mtsogoleri wa mpingo wa akatolika pa dziko lonse lapansi Papa Francis walangiza akhristu kuti asaononge makobiri mu nyengo yokumbukira kubadwa kwa Ambuye Yesu. Papa walankhula izi ku likulu la mpingo wa katolika ku Vatican. Ndipo mukulankhula kwake, iye wanena kuti anthu agwirise ntchito ena mwa makobiri awo pothandiza anthu amene akuvutika ndi nkhondo ku Ukraine. […]

The post Khirisimisi isakuloweni mnthumba – atero Papa appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください