A nthambi ya ndende ati vuto la chakudya lachepa tsopano

Mneneri wa nthambi ya ndende a Chimwemwe Shaba ati pakadali pano tsopano vuto lakusowa kwa chakudya mu ndende lachepa chifukwa ali ndi chakudya maka chimanga chomwe chikhoza kuwafikitsa mu March chaka chamawa. Malingana ndi a Shaba, Boma lalowererapo pothetsa vuto lachakudya lomwe linalipo mndende za mdziko lino pofunsa bungwe la Admarc kuti ligulitse matumba 25,000 […]

The post A nthambi ya ndende ati vuto la chakudya lachepa tsopano appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください