Siyani kudya gondolosi musanakule – APM

Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika wauza achinyamata kuti asamadye nawo gondolosi pofuna kuonjezera mphamvu. Iye wanena izi pa mwambo wa Mulhakho wa Alhomwe kwa Chonde mu boma la Mulanje. Polangiza achinyamata kuti akhale ndi moyo wautali monga iye, Mutharika anati achinyamata asiye kugwiragwira. “Ine ndinafika pano chifukwa cha zinthu zingapo. Ndimapewa kugwiragwira, […]

The post Siyani kudya gondolosi musanakule – APM appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください