Yemwe adanena kuti khoswe wapadzala anaulura wapatsindwi adadziwa kuti tsiku lina oyimba Patience Namadingo adzakana chitonzo choti anadya ndalama zothandizira odwala ndipo m’malo mwake ndikuulura kuti iye ndi yemwe analeletsa ndalamazi mmanja mwa akuluakulu a chipatala cha Queen Elizabeth omwe wati ankafuna kuzidya. Nkhaniyi inayamba mchaka cha 2017 pomwe Namadingo anadzipeleka kuti asaka ndalama yokwana […]
The post Fisi anakana nsatsi: Namadingo waloza chala akuluakulu a Qech pa K15 miliyoni appeared first on Malawi 24.