Misonkho ya a Malawi: Ma alawasi abowoka ku UNGA

Pomwe a Malawi ochuluka akudandaula za mavuto adzaoneni pankhani ya zachuma, anthu omwe aperekeza mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ku nsonkhano wamayiko (UNGA), akhala akupuma moyo wina akabwera kumudzi kuno, pomwe malipoti akusonyeza kuti anthuwa apatsidwa ma alawasi anyo! Malingana ndi nyuzipepala ya Malawi News yomwe yatulutsidwa lero pa 17 September, 2022, ofeso […]

The post Misonkho ya a Malawi: Ma alawasi abowoka ku UNGA appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください