Kampani yofulula mowa ya Castel yalengeza kuti mitengo ya zakumwa zawo zoiwalitsa mavuto amene dziko lino likukumana nawo azikweza. Ati kuyambila mawa, mowa ukhala okwelelako mtengo. Malinga ndi chikalata chomwe kampaniyi yatulutsa, mitengo ya mowa ikukwela kamba ka kukwela mitengo ya zinthu mu dziko muno. “Takakamizika kukweza mitengo kamba ka kusintha kwa mitengo mu dziko […]
The post Chakumwa nacho Chakwera appeared first on Malawi 24.