Bola kwa Farao: Afrobarometer yati a Malawi ochuluka atha kuvotela DPP

Ngati mu chipululu nthawi ya Mose, khamu la a Malawi likuti bola ku Aiguputo komkuja. Ulendo wa ku Kenani otsogoleledwa ndi Tonse uja ukuoneka waomba khoma. Tsogolo palibe. Utsogoleri wake ndi opatsa khambi. Kafukufuku amene bungwe la Afrobarometer anachita mu mwezi wa February, ati anaonetsa kuti a Malawi ochuluka ndi okonzeka kuvotelanso chipani cha DPP. […]

The post Bola kwa Farao: Afrobarometer yati a Malawi ochuluka atha kuvotela DPP appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください