Chepetsani uchimo wa uchidakwa — Simama

Bishop Abraham Simama wa Mpingo wa Glorious Light International wa mzinda wa Lilongwe wadandaula ndi mchitidwe wauchidakwa omwe wachulukira pakati pa achinyamata mu dziko lino. Poyankhula pa msonkhano wa tolankhani lachinayi, a Simama anati mpingowu waganiza zopanga msonkhano wachinyamata omwe udzachitikire ku malo opembedzera ku Lilongwe. A Bishop Simama adauza atolankhani kuti achinyamata amasikuano ali […]

The post Chepetsani uchimo wa uchidakwa — Simama appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください