Anabwela atayaka kapena? A Kongeresi ati za mgwilizano amayankhula Chilima ndi zamkutu

Zija amayankhula wachiwili kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima zoti anagwilizana ndi a Lazarus Chakwera kulandilana mu 2025 ati ndi zamkutu komanso zongopeka. A Kongeresi alibe mgwilizano umenewo. Malingana ndi mlembi wamkulu wa chipani cha Kongeresi, a Eisenhower Mkaka, chipani cha MCP chilibe ma pepala a mgwilizano amene akukamba a Chilima. Iwo anena […]

The post Anabwela atayaka kapena? A Kongeresi ati za mgwilizano amayankhula Chilima ndi zamkutu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です