Onesimus wavomereza kuti ananyula usiku wa loweruka pomwe ananyoza amuna. Woyimbayu wati sadzayambiranso ndipo wapempha kuti anthu amukhululukire . Woyimbayu yemwe ena amamuti Chintuwi watulutsa uthenga wake opepesa a Malawi. Loweruka ku mwambo wa zoyimbayimba osangalala za mowa wa kuchekuche ku Lilongwe, Onesimus ananyogodola amuna omwe omwe sapatsa akazi awo ndalama ponena kuti amunawa ndi […]
The post Ndinanyula – Onesimus appeared first on Malawi 24.