Chakwera, Chilima akukaipatsa moto Flames

Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera, pamodzi ndi wachiwili wake Saulos Chilima, alengeza kuti akaonera nawo mpira wapakati pa timu ya dziko lino ndi Ethiopia pa bwalo la Bingu lamulungu lino. Izi ndimalingana ndi chikalata chomwe boma latulutsa lachisanu chomwe chimafotokoza mndandanda wamomwe a Chakwera agwilire ntchito kumathero a sabatayi komaso kumayambiliro a sabata ya […]

The post Chakwera, Chilima akukaipatsa moto Flames appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です