Gomani awuza Chakwera kuti achotse ntchito omunamiza

Mfumu yaikulu ya angoni a kwa Maseko am’boma la Ntcheu, Inkosi ya Makosi Gomani yachisanu, yawuza mtsogoleri wadziko lino a Lazarus Chakwera kuti achotse mmaudindo onse omwe akumamunamiza komaso omwe sakugwira bwino ntchito yawo. Inkosi ya Makosi Gomani yachisanuyi imayankhula izi lolemba ku Ntcheu pa msonkhano wa chitukuko omwe mtsogoleri wa dziko linoyu anachititsa atamaliza […]

The post Gomani awuza Chakwera kuti achotse ntchito omunamiza appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です