Zauchifwamba zitha kuchitika ku Malawi, boma la UK lachenjeza

Boma la United Kingdom lachenjeza kuti anthu ena ayesera kuchita zauchifwamba kuno ku Malawi. Mu uthenga wa pa intaneti, dzikoli lauza nzika zake kuti zisapite ku Malawi chifukwa cha chiopsezo cha ziwawazi. Langizio la zauchifwambazi ladza potengera zomwe lapeza bungwe lomwe limayang’ana za zauchifwamba ndi uchigawenga ku UK ko. “Pali chiopsezo  choti nthu ena a […]

The post Zauchifwamba zitha kuchitika ku Malawi, boma la UK lachenjeza appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です