Boma la Malawi kudzera kuunduna wa zamalonda lati chimodzi mwa zinthu zomwe zapangitsa kuti mitengo ya zinthu ikwere mdziko muno ndi nkhondo yapakati pa dziko la Russia komaso Ukraine yomwe akuti yasokoneza ntchito za malonda padziko lonse. Izi ndi malingana ndi nduna yoona za malonda a Mark Katsonga komaso nduna yazofalitsa nkhani a Gospel Kazako […]
The post Nkhondo ya Russia, Ukraine yakhudza mitengo yazinthu kuno – boma appeared first on Malawi 24.