Ophunzira 3 million salemba mayeso ku Sri Lanka, boma likukanika kugula mapepala

Olemba: Gracious Zinazi Dziko la Sri Lanka lomwe linachita malire ndi dziko la India latsimikiza kuti ana a sukulu pafupifupi 3 million salemba mayeso chifukwa dzikoli likukumana ndi mavuto a zachuma ndipo silingakwanitse kugula mapepala. Boma la dzikoli lilibe ndalama zosindikizira komanso kugulira mapepala opangira mayeso chifukwa chakusowa kwa ndalama zakunja maka mu mzinda waukulu […]

The post Ophunzira 3 million salemba mayeso ku Sri Lanka, boma likukanika kugula mapepala appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です