M’modzi mwa oyimba odziwika bwino mdziko muno yemweso ndi m’busa, Mlaka Maliro, wati nkhani zomwe anthu akufalitsa zokhudza mkazi wake Bernadetta ndizabodza ndipo waopseza kuti athana ndi aliyese olimbana ndi mkazi wakeyo. Nkhaniyi ikubwera kutsatira kutula pasi udindo kwa a Maliro ngati m’busa wa mpingo wa ECG Jesus Nation omwe mwini wake ndi mneneri Shepherd […]
The post Chili chonse chomwe mwamva chokhudza mkazanga ndibodza – Mlaka Maliro appeared first on Malawi 24.