Wolemba: Gracious Zinazi Pamene a Malawi akuonetsa kuti anailandira mwa chimwemwe sevisi ya Pamtsetse kuchokera ku TNM komanso MoFaya kuchokera ku Airtel Malawi Plc, zadziwika kuti masevisiwa ndi a miyezi itatu yokha. Izi zatsimikizika pomwe kampani ya Airtel Malawi Plc yatulutsa chidziwitso komanso kulemba pa tsamba lake la mchenzo la Twitter pomwe imayankha mmodzi mwa […]
The post Pamtsetse ndi MoFaya sanabwere kuzakhala appeared first on Malawi 24.