Mabishopu a Chikatolika adzudzula mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kuti akumachedwa kumanga mfundo maka pa nkhani yothana ndi katangale ngakhale kuti ali ndi mphamvu zowalora kuchita zinthu mu nthawi yake. Mabishopuwa anena izi mu kalata yomwe atulutsa lero ndipo yasayinidwa ndi mabishopu asanu ndi awiri a mdziko lino. Mu kalatayi, ma bishopu ati […]
The post Utsogoleri wa Boma la Tonse ndi wofooka – atero mabishopu appeared first on Malawi 24.