30 billion ya AIP sinadyedwe ndi chi Aviator, koma mwina 1 billion yokha – boma latero

A unduna wa zamalimidwe atsutsa maripoti oti akathyali ena anawachenjeretsa ndalama zokwana 30 billion za fetereza otchipa. Malinga ndi maripoti amene atchuka, ati ma dobadoba ena a ku United Kingdom anatsekula mmaso boma la a Chakwera polidyera 30 billion ya ndondomeko ya AIP. Maripotiwa ati kampani ina ya dziko la UK inalonjeza kubweretsa fetereza ku […]

The post 30 billion ya AIP sinadyedwe ndi chi Aviator, koma mwina 1 billion yokha – boma latero appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください